10 Ndipo Mose anawauza, ndi kuti, Pakutha pace pa zaka zisanu ndi ziwiri, pa nyengo yoikika ya m'caka cakulekerera, pa madyerero a misasa;
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 31
Onani Deuteronomo 31:10 nkhani