19 Ndipo tsopano mudzilemberere nyimbo iyi, ndi kuphunzitsa ana a Israyeli iyi: mulike m'kamwa mwao, kuti nyimbo iyi indicitire mboni yotsutsa ana a Israyeli.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 31
Onani Deuteronomo 31:19 nkhani