Deuteronomo 31:27 BL92

27 Pakuti ndidziwa kupikisana kwanu, ndi kupulukira kwanu; taonani, pokhala ndikali ndi moyo pamodzi ndi inu lero, mwapikisana ndi Yehova: koposa kotani nanga nditamwalira ine!

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 31

Onani Deuteronomo 31:27 nkhani