Deuteronomo 31:6 BL92

6 Khalani amphamvu, limbikani mitima, musamacita mantha, kapena kuopsedwa cifukwa ca iwowa; popeza Yehova Mulungu wanu ndiye amene amuka nanu; iye sadzakusowani, kapena irukusiyani.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 31

Onani Deuteronomo 31:6 nkhani