8 Ndipo Yehova, iye ndiye amene akutsogolera; iye adzakhala ndi iwe, iye sadzakusowa kapena kukusiya; usamacita mantha, usamatenga nkhawa.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 31
Onani Deuteronomo 31:8 nkhani