2 Ciphunzitso canga cikhale ngati mvula;Maneno anga agwe ngati mame;Ngati mvula yowaza pamsipu,Ndi monga madontho a mvula pazitsamba.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 32
Onani Deuteronomo 32:2 nkhani