35 Kubwezera cilango nkwanga, kubwezera komwe,Pa nyengo ya kuterereka phazi lao;Pakuti tsiku la tsoka lao layandika,Ndi zinthu zowakonzeratu zifulomira kudza.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 32
Onani Deuteronomo 32:35 nkhani