Deuteronomo 32:39 BL92

39 Tapenyani tsopano kuti Ine ndine iye,Ndipo palibe mulungu koma Ine;Ndipha Ine, ndikhalitsanso ndi mayo:Ndikantha, ndicizanso Ine;Ndipo palibe wakulanditsa m'dzanja langa.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 32

Onani Deuteronomo 32:39 nkhani