43 Kondwerani, amitundu inu, ndi anthu ace;Adzalipsira mwazi wa atumiki ace,Adzabwezera cilango akumuukira,Nadzafafanizira zoipa dziko lace, ndi anthu ace.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 32
Onani Deuteronomo 32:43 nkhani