Deuteronomo 32:51 BL92

51 popeza munandilakwira pakati pa ana a Israyeli ku madzi a Meriba wa Kadesi m'cipululu ca Zini, popeza simunandipatula Ine pakati pa ana a Israyeli,

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 32

Onani Deuteronomo 32:51 nkhani