Deuteronomo 33:16 BL92

16 Ndi zinthu zofunikatu za dziko lapansi, ndi kudzala kwace,Ndi cibvomerezo ca iye anakhala m'citsambayo;Mdalitso ufike pa mutu wa Yosefe,Ndi pakati pa mutu wace wa iye wokhala padera ndi abale ace.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33

Onani Deuteronomo 33:16 nkhani