19 Adzaitana mitundu ya anthu afike kuphiri;Apo adzaphera nsembe za cilungamo;Popeza adzayamwa zocuruka za m'nyanja,Ndi cuma cobisika mumcenga.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33
Onani Deuteronomo 33:19 nkhani