23 Za Nafitali anati,Nafitali, wokhuta nazo zomkondweretsa,Wodzala ndi mdalitso wa Yehova;Landira kumadzulo ndi kumwela.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33
Onani Deuteronomo 33:23 nkhani