2 Musamaonjeza pa mau amene ndikuuzani, kapena kucotsapo, kuti musunge malamulo a Yehova Mulungu wanu, amene ndikuuzani.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 4
Onani Deuteronomo 4:2 nkhani