Deuteronomo 4:29 BL92

29 Koma mukafuna Yehova Mulungu wanu kumeneko, mudzampeza, ngati mumfunafuna ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 4

Onani Deuteronomo 4:29 nkhani