Deuteronomo 4:32 BL92

32 Pakuti, funsiranitu, masiku adapitawo, musanakhale inu, kuyambira tsikuli Mulungu analenga munthu pa dziko lapansi, ndi kuyambira malekezero ena a thambo kufikira malekezero anzace a thambo, ngati cinthu cacikuru conga ici cinamveka, kapena kucitika?

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 4

Onani Deuteronomo 4:32 nkhani