43 ndiyo Bezere, m'cipululu, m'dziko lacidikha, ndiwo wa Anrubeni; ndi Ramoti m'Gileadi, ndiwo wa Agadi; ndi Golani, m'Basana, ndiwo wa Amanase.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 4
Onani Deuteronomo 4:43 nkhani