16 Lemekeza atate wako ndi amako, monga Yehova Mulungu wako anakulamulira; kuti masiku ako acuruke, ndi kuti cikukomere, m'dziko limene Yehova Mulungu wako akupatsa iwe.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 5
Onani Deuteronomo 5:16 nkhani