Deuteronomo 5:22 BL92

22 Yehova ananena mau awa kwa msonkhano wanu wonse, m'phirimo ali pakati pa moto, pamtambo, pamdima bii, ndi mau akuru; osaonjezapo kanthu. Ndipo anawalembera pa magome awiri amiyala, nandipatsa awa.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 5

Onani Deuteronomo 5:22 nkhani