Deuteronomo 5:3 BL92

3 Yehova sanacita cipangano ici ndi makolo athu, koma ndi ife, ife amene tiri ndi moyo tonsefe pane lero.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 5

Onani Deuteronomo 5:3 nkhani