31 Koma iwe, uime kuno ndi Ine, ndinene ndi iwe malamulo onse, ndi malemba, ndi maweruzo, amene uziwaphunzitsa, kuti awacite m'dziko limene ndiwapatsa likhale lao lao.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 5
Onani Deuteronomo 5:31 nkhani