17 Muzisunga mwacangu malamulo a Yehova Mulungu wanu, ndi mboni zace, ndi malemba ace, amene anakulamulirani.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 6
Onani Deuteronomo 6:17 nkhani