Deuteronomo 6:25 BL92

25 Ndipo kudzakhala kwa ife cilungamo, ngati tisamalira kucita malamulo awa onse pamaso pa Yehova Mulungu wathu, monga anatilamuliraife.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 6

Onani Deuteronomo 6:25 nkhani