Deuteronomo 7:12 BL92

12 Ndipo kudzakhala, cifukwa ca kumvera inu maweruzo awa, ndi kuwasunga, ndi kuwacita, Yehova Mulungu wanu adzakusungirani cipangano ndi cifundo cimene analumbirira makolo anu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7

Onani Deuteronomo 7:12 nkhani