Deuteronomo 7:2 BL92

2 nakawapereka Yehova Mulungu wanu pamaso panu, ndipo mukawakanthe; pamenepo muwaononge konse; musapangana nao pangano, kapena kuwacitira cifundo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7

Onani Deuteronomo 7:2 nkhani