Deuteronomo 7:9 BL92

9 Cifukwa cace dziwani kuti Yehova Mulungu wanu ndiye Mulungu; ndiye Mulungu wokhulupirika, wakusunga cipangano ndi cifundo ndi iwo akumkonda ndi kusunga malamulo ace, kufikira mibadwo zikwi.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7

Onani Deuteronomo 7:9 nkhani