Deuteronomo 8:1 BL92

1 Muzisamalira kucita malamulo onse amene ndikuuzani lero lino, kuti mukhale ndi moyo, ndi kucuruka, ndi kulowa, ndi kulandira dziko limene Yehova analumbirira makolo anu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 8

Onani Deuteronomo 8:1 nkhani