Deuteronomo 8:9 BL92

9 dziko loti mudzadyamo mkate wosapereweza; simudzasowamo kanthu; dziko loti miyala yace nja citsulo, ndi m'mapiri ace mukumbe mkuwa.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 8

Onani Deuteronomo 8:9 nkhani