Deuteronomo 9:1 BL92

1 Imvani Israyeli; mulikuoloka Yordano lero lino, kulowa ndi kulandira amitundu akuru ndi amphamvu akuposa inu, midzi yaikuru ndi ya malinga ofikira kuthambo,

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 9

Onani Deuteronomo 9:1 nkhani