Deuteronomo 9:12 BL92

12 Ndipo Yehova anati kwa ine, Uka, fulumira kutsika kuno popeza anthu ako unawaturutsa m'Aigupto wa anadziipsa; anapatuka msanga m'njira ndinawalamulirayi; anadzipangira fano loyenga.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 9

Onani Deuteronomo 9:12 nkhani