7 Kumbukilani, musamaiwala, kuti munakwiyitsa Yehova Mulungu wanu m'cipululu; kuyambira tsikuli munaturuka m'dziko la Aigupto, kufikira munalowa m'malo muno munapiktsana ndi Yehova.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 9
Onani Deuteronomo 9:7 nkhani