12 Ndipo Kalebe anati, iye amene akantha mudzi wa Seferi, naulanda, yemweyo ndidzampatsa Akisa mwana wanga wamkazi akhale mkazi wace.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 1
Onani Oweruza 1:12 nkhani