13 Ndipo Otiniyeli, mwana wa Kenazi mng'ono wa Kalebi anaulanda, ndipo anampatsa Akisa mwana wace wamkazi akhale mkazi wace.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 1
Onani Oweruza 1:13 nkhani