17 Ndipo Yuda anamuka ndi Simeoni mkuru wace, nakantha Akanani akukhala m'Zefati, nauononga konse. Koma dzina la mudziwo analicha Horima.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 1
Onani Oweruza 1:17 nkhani