18 Yuda analandanso Gaza ndi malire ace, ndi Asikeloni ndi malire ace, ndi Ekroni ndi malire ace.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 1
Onani Oweruza 1:18 nkhani