19 Ndipo Yehova anali ndi Yuda, iye nawaingitsa a kumapiri, osaingitsanzika za kucigwa, popeza zinali nao magareta acitsulo.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 1
Onani Oweruza 1:19 nkhani