Oweruza 1:3 BL92

3 Ndipo Yuda ananena ndi Simeoni mkuru wace, Kwera nane ku gawo langa kuti tiwathire nkhondo Akanani; ndipo inenso ndidzamuka nawe ku gawo lako. Namuka naye Simeoni.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 1

Onani Oweruza 1:3 nkhani