Oweruza 11:19 BL92

19 Ndipo Israyeli anatuma mithenga kwa Sihoni mfumu ya Aamori, mfumu ya ku Hesiboni; nanena naye Israyeli, Tikupemphani tipitire pakati pa dziko lanu, kumka kwathu.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 11

Onani Oweruza 11:19 nkhani