Oweruza 11:25 BL92

25 Ndipo tsopano kodi inu ndinu wabwino woposa Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Moabu; anatengana konse ndi Israyeli iyeyu kodi, kapena kucita nao nkhondo konse kodi?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 11

Onani Oweruza 11:25 nkhani