Oweruza 11:26 BL92

26 Pokhala Israyeli m'Hesiboni ndi midzi yace, ndi m'Aroeri ndi midzi yace, ndi m'midzi yonse yokhala m'mphepete mwa Arinoni zaka mazana atatu; munalekeranji kulandanso nthawi ija?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 11

Onani Oweruza 11:26 nkhani