Oweruza 11:33 BL92

33 nawakantha kuyambira ku Aroeri mpaka ufika ku Miniti, ndiyo midzi makumi awiri, ndi ku Abelikerami, makanthidwe akuru ndithu. Motero ana a Amoni anagonjetsedwa pamaso pa ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 11

Onani Oweruza 11:33 nkhani