Oweruza 11:34 BL92

34 Pofika Yefita ku Mizipa ku nyumba yace, taonani, mwana wace wamkazi anaturuka kudzakomana naye ndi malingaka ndi kuthira mang'ombe; ndipo iyeyu anali mwana wace mmodzi yekha, analibe mwana wina wamwamuna kapena wamkazi.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 11

Onani Oweruza 11:34 nkhani