37 Ndipo anati kwa atate wace, Andicitire ici, andileke miyezi iwiri, kuti ndicoke ndi kutsikira kumapiri, ndi kulirira unamwali wanga, ine ndi anzanga.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 11
Onani Oweruza 11:37 nkhani