Oweruza 11:7 BL92

7 Ndipo Yefita anati kwa akulu a Gileadi, Simunandida kodi, ndi kundicotsa m'nyumba ya atate wanga? ndipo mundidzeraoji tsopano pokhala muli m'kusauka?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 11

Onani Oweruza 11:7 nkhani