Oweruza 11:9 BL92

9 Ndipo Yefita anati kwa akuru a Gileadi, Mukaodifikitsanso kwathu kucita nkhondo ndi ana a Amoni, nakawapereka Yehova pamaso panga, ndidzakhala mkuru wanu kodi?

Werengani mutu wathunthu Oweruza 11

Onani Oweruza 11:9 nkhani