Oweruza 12:6 BL92

6 pamenepo anati kwa iye, Unene tsono Shiboleti; ndipo akati, Siboleti, osakhoza kuchula bwino, amgwira namupha padooko pomwe pa Yordano; ndipo anagwa a Efraimu nthawi ija, zikwi makumi anai mphambu ziwiri.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 12

Onani Oweruza 12:6 nkhani