Oweruza 12:9 BL92

9 Ndipo anali nao ana amuna makumi atatu; ndi ana akazi makumi atatu anawakwatitsa kwina, natengera ana ace amuna ana akazi makumi atatu ocokera kwina. Ndipo anaweruza Israyeli zaka zisanu ndi ziwiri.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 12

Onani Oweruza 12:9 nkhani