8 Pamenepo Manowa anapembedza Yehova, nati, Yehova, ndikupemphani, atidzerenso munthu wa Mulungu mudamtumayo, natilangize ico tizicitira mwanayo akadzabadwa.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 13
Onani Oweruza 13:8 nkhani