Oweruza 14:12 BL92

12 Nanena nao Samsoni, Mundilole ndikuphereni mwambi; mukanditanthauziratu uwu m'masiku asanuwa a madyerero, ndi kuukumika uwu, ndidzakupatsani malaya a nsaru yabafuta makumi atatu, ndi zobvala zosinthanitsa makumi atatu;

Werengani mutu wathunthu Oweruza 14

Onani Oweruza 14:12 nkhani