Oweruza 14:17 BL92

17 Ndipo analira pamaso pace masiku asanu ndi awiriwo pocitika madyerero ao; koma kunali kuti tsiku lacisanu ndi ciwiri anamuuza, popeza anamuumiriza; ndipo anatanthauzira anthu a mtundu wace mwambiwo.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 14

Onani Oweruza 14:17 nkhani